Willz Mr Nyopole - Ndimaku pempelelako lyrics

[Willz Mr Nyopole - Ndimaku pempelelako lyrics]

Ndimaku, kuku, ndimaku, "phat jam records "
Kuku, ndimaku pempelelako
Ndimaku pempelelako

Ndimaku pempelelako chauta anke wako
Kuti upedza wako okonda mutima wako
Ndimaku pempelelako
Unga kale unayenda unanisiya
Ndimaku pempelelako mulungu eka ndiye aziwa
Ndimaku pempelelako sikulina ndiza pola
Ndimaku pempelelako

Hello! Hello! Kodi unakwanisa
Zipeza zimene unalu sakila Mu chikondi?
Nimango zifunsa ma funso kodi anaku pasa
Zimeni ninalepela kuku pasa?
Kodi ninalakwa chani?
Unango nisiya ko panda chifukwa
Ma ma ma, Natangwa nika kumbukila mau yako
Yochoka pakamwa kako unati sunga yende
Ngakale Mabvuto achuluke

Ndimaku pempelelako chauta anke wako
Kuti upedza wako okonda mutima wako
Ndimaku pempelelako
Unga kale unayenda unanisiya
Ndimaku pempelelako mulungu eka ndiye aziwa
Ndimaku pempelelako sikulina ndiza pola
Ndimaku pempelelako

Iye Iye kodi umamudza umu konda?
Kodi mutima wako una kondwa?
Kodi ukamu langa mumaso umanva chikondi
Chochoka pansi pamutima?
Kodi suzamusiya naye?
Kodi uzaka kalamba naye?
Kodi ntawi zina mwina umaganizapo
Kuti wenane tinga bwezane?
Kodi unga kondwele nazo
Mwina inga nkale Mphatso?
Ayo ndima ganizo yanga anyway

Ndimaku pempelelako chauta anke wako
Kuti upedza wako okonda mutima wako
Ndimaku pempelelako
Unga kale unayenda unanisiya
Ndimaku pempelelako mulungu eka ndiye aziwa
Ndimaku pempelelako sikulina ndiza pola
Ndimaku pempelelako

Ndimaku pempelelako chauta anke wako
Kuti upedza wako okonda mutima wako
Ndimaku pempelelako
Unga kale unayenda unanisiya
Ndimaku pempelelako mulungu eka ndiye aziwa
Ndimaku pempelelako sikulina ndiza pola
Ndimaku pempelelako

Phat jam records

Interpretation for


Add Interpretation

Add extended interpretation

If you know what the artist is talking about, can read between the lines, and know the history of the song, you can add interpretation to the lyrics. After checking by our editors, we will add it as the official interpretation of the song!

Latest added interpretations to lyrics

A B C D E F G H I J K L M N O P Q R S T U V W X Y Z #
Interpret