Jeg Tellem - Mtopola lyrics
[Jeg Tellem - Mtopola lyrics]
Ah Hee yeah hee
Mukukamba zinkhani zambiri
Mukafuna ndiwononge mbiri kodi nchikondi
Ndimayesa tilimo awiri
Muli ndi nthawi muli busy chonde msachimwise
Ayi nsadanise ndi wangayu
Achuluka anthu okhomelela ahahaha
Kankhani pang'ono kukhomelela koma why
ATI ndingofuna ndingokudyela ineyo
Atumapo anthu kuzandikwenya ndee tinamenyana
Mumvetse olo mu dameje dameje
Kumuleka sizingatheke ndimadana ndi mtopola
Muleke zomakamuwuza miseche
Ndicholinga choti athese
Ndimadana ndi mtopola
Ine ndimadana ndi mtopola mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola ndimadana ndi mtopola
Ndati ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola
Yeah umaganiza bwanji kukwatira beast
Iweyo ndi Ka beauty ofunika Prince
Mamuna Oti nthumba anathila yeast
Osati kafinyanya wonunkha gilisi
Mhuu koma mtopola
Ndizamumveso wina nzamunokola
Kumawuza anzake andisomphola
Ndizamponda pamutu ndi chigogoda
Cell nzalowa Bola ndamtchola
Eya pezani zina zochita
Eya kupeza wanu nzovuta
Eya mungomupempha Chauta osativuta
Mwachuluka anthu okhomelela
Kankhani pang'ono kupemelela
ATI ndingofuna ndingokudyela
Koma tizamenyana
Mumvetse olo mu dameje dameje
Kumuleka sizingatheke ndimadana ndi mtopola
Muleke zomakamuwuza miseche
Ndicholinga choti athese
Ndimadana ndi mtopola
Ine ndimadana ndi mtopola mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola ndimadana ndi mtopola
Ndati ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola olo mu dameje dameje
Kumuleka sizingatheke
Olo mumuwuze miseche yeah ey yeah
Yeah ey yeah ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola
Ndati ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola ndimadana ndi mtopola